Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 1/14 tsamba 4
  • Zochitika mu Utumiki Wakumunda

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zochitika mu Utumiki Wakumunda
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 1/14 tsamba 4

Zochitika mu Utumiki Wakumunda

M’mwezi wa September 2013, alongo 9 ochokera mu mpingo wa Lilongwe English anapita kukalalikira m’gawo la mpingo wa Ntcheu Central kwa mlungu umodzi ataloledwa ndi ofesi ya nthambi. Alongowa ankayamba kulalikira 5:30 m’mawa mpaka 6:30 madzulo. Pa mlungu umene anakhala kumeneku, analalikira maola 625 ndipo anagawira magazini 4,048. Alongowa anayamikira kwambiri mmene abale ndi alongo a mpingo wa Ntcheu Central anawathandizira polowa nawo mu utumiki komanso pa zinthu zina. Zimene alongowa anachita ndi zogwirizana ndi zimene timawerenga pa Salimo 110:3 kuti: “Anthu ako adzadzipereka mofunitsitsa pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.” Apa zikuonekeratu kuti mtima wodzipereka ndi chizindikiro cha Akhristu oona.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena