Magazini Yophunzira
July 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 3-30, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
BULGARIA
Chithunzichi akuyerekezera zimene zimachitika pophunzitsa Baibulo anthu amene ali kundende m’dziko la Bulgaria
KULI OFALITSA
2,475
MAPHUNZIRO A BAIBULO
2,950
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2017)
5,327
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa webusaiti yathu ya www.jw.org/ny
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.