Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w16 December tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
w16 December tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

3 Mbiri ya Moyo Wanga​—Ndayesetsa Kukhala “Zinthu Zonse kwa Anthu Osiyanasiyana”

MLUNGU WA JANUARY 30, 2017–FEBRUARY 5, 2017

8 Tinamasulidwa ku Uchimo Chifukwa cha Kukoma Mtima Kwakukulu

MLUNGU WA FEBRUARY 6-12, 2017

13 “Kuika Maganizo pa Zinthu za Mzimu Kumabweretsa Moyo ndi Mtendere”

M’buku la Aroma chaputala 6 ndi 8, muli mfundo zothandiza kwambiri Akhristufe. Machaputala amenewa atithandiza kuti tizipindula ndi kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu komanso kuti tiziika maganizo athu pa zinthu zimene zingatibweretsere madalitso amuyaya.

18 Kodi Mukukumbukira?

MLUNGU WA FEBRUARY 13-19, 2017

19 Muzimutulira Yehova Nkhawa Zanu Zonse

MLUNGU WA FEBRUARY 20-26, 2017

24 Yehova Amapereka Mphoto kwa Anthu Omufunafuna ndi Mtima Wonse

Nkhani yoyambayi ikufotokoza zimene tingachite kuti titulire Yehova nkhawa zathu. Nkhani yachiwiri ikusonyeza kuti chikhulupiriro chathu chimalimba ngati sitikayikira zoti Yehova amapereka mphoto kwa anthu amene amamufunafuna ndi mtima wonse. Ikusonyezanso kuti madalitso amene Yehova watilonjeza amatithandiza kuti tikhalebe okhulupirika.

29 Munthu Wofatsa Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru

32 Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2016

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena