Zamkatimu
June 1, 2011
Kodi Ndani Adzathetse Umphawi?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Anthu Ena Ali pa Umphawi Wadzaoneni
4 Zimene Ena Achita Pofuna Kuthetsa Umphawi
7 Nkhani Yabwino Kwa Anthu Osauka
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Akufa Adzauka?
19 Yandikirani Mulungu—Nkhani Yolimbikitsa Kwa Anthu Osweka Mtima
24 Kalata Yochoka ku Madagascar
26 Phunzitsani Ana Anu—Kodi Umaona Kuti Ana Anzako Safuna Kucheza Nawe?
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
9 Kodi Mungatani Kuti Muzigula Zinthu Mogwirizana Ndi Ndalama Zimene Mumapeza?
13 Kodi Mulungu Ali Ndi Gulu Lake Limene Akulitsogolera?
20 Kodi Baibulo Linalembedwa Liti?
28 Ndinkafunitsitsa Kudzagwira Ntchito Yoyenda M’madera Osiyanasiyana
32 “Kodi Anthu Saliwonongeratu Dziko Lapansili?”