Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w09 7/1 tsamba 32
  • Tsamba 32

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tsamba 32
  • Nsanja ya Olonda—2009
Nsanja ya Olonda—2009
w09 7/1 tsamba 32

Tsamba 32

◼ Kodi ndi ndani amene angakuthandizeni kuti mumvetse bwino Baibulo? Onani masamba 6 mpaka 8.

◼ Kodi n’zotheka kukhala ndi mtendere m’dziko la mavutoli? Onani masamba 10 mpaka 12.

◼ Kodi anthu apezadi chingalawa cha Nowa? Onani masamba 13 ndi 14.

◼ Kodi Abigayeli anali ndani, ndipo ifeyo tingaphunzirepo chiyani pa chikhulupiriro chake? Onani masamba 18 mpaka 21.

◼ Kodi Mulungu amavomereza mitala? Onani tsamba 30.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena