Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w01 4/1 tsamba 32
  • Mwambo Womwe Simuyenera Kuphonya

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mwambo Womwe Simuyenera Kuphonya
  • Nsanja ya Olonda—2001
Nsanja ya Olonda—2001
w01 4/1 tsamba 32

Mwambo Womwe Simuyenera Kuphonya

“Mphatso iliyonse yabwino, ndi chininkho chilichonse changwiro” zimachokera kwa Mulungu, Atate wathu wakumwamba.​—Yakobo 1:17.

MPHATSO yaikulu kwambiri yomwe wapereka kwa anthu ochimwa ndiyo makonzedwe akuti anthuwo apulumutsidwe mwa Mwana wake wobadwa yekha, Yesu Kristu. Imfa ya Yesu, Momboli wathu, inapangitsa moyo wosatha padziko lapansi kukhala wotheka. Pa Luka 22:19, timalamulidwa kukumbukira imfa yake.

Mboni za Yehova zikukupemphani mwachikondi kuti mukakhale nazo pamodzi posunga lamulo la Yesu limeneli. Mwambo wapachaka umenewu udzachitika dzuŵa litaloŵa padeti logwirizana ndi Nisani 14 pa kalendala yoyendera mwezi ya Baibulo, lomwe ndi Lamlungu, April 8, 2001. Sungani deti limeneli kuti musadzaiŵale. Mboni za Yehova za m’dera lanu zingakuuzeni malo ake enieni ndi nthaŵi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena