Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?
Ngakhale m’dziko lino lodzala ndi mavuto, mukhoza kupeza chimwemwe m’chidziŵitso cholongosoka cha m’Baibulo chonena za Mulungu, Ufumu wake, ndi chifuno chake chodabwitsa kaamba ka anthu. Ngati mungafune chidziŵitso chowonjezereka kapena ngati mungakonde kuti wina akabwere kudzachita nanu phunziro Labaibulo lapanyumba laulere, chonde lemberani Watch Tower, Box 21598, Kitwe, kapena ku keyala yoyenerera yondandalitsidwa patsamba 2.