Iye “Anamenya Nkhondo Yabwino”
Mbale F. E. Skinner anamaliza ntchito yake ya padziko lapansi pa July 4, 1990. Edwin Skinner anali ndi zaka 96 zakubadwa ndipo anatumikira zikondwerero Zaufumu wa Yehova kwa nthaŵi zonse mu India chiyambire July 1926. Iye anabatizidwira ku Mangalande mu 1919. Mbiri ya moyo wake inalembedwa mu Nsanja ya Olonda ya January 1, 1990. Mbale Skinner analidi mwamuna wachikhulupiriro ndi chipiriro m’kuyenda panjirayo kufikira mapeto, ndipo iye wapezadi mphotho yake.—2 Timoteo 4:7, 8, NW.