Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w90 10/1 tsamba 32
  • Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?
  • Nsanja ya Olonda​—1990
Nsanja ya Olonda​—1990
w90 10/1 tsamba 32

Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?

Kodi Yesu Kristu Ali Mulungu Wamphamvuyonse?

Munthu wa ku Hayward, California, akulemba motere: “Ndine wochititsidwa chidwi, wosangalatsidwa, ndi wokondweretsedwa ndi broshuwa yotchulidwa pamwambayo. Iyo ndi bukhu la akatswiri londandalitsa chidziŵitso kuchokera m’magwero osiyanasiyana achipembedzo ndi kugwira mawu ovomereza kuti chiphunzitso cha Utatu n’chonyenga, chosokeretsa, ndipo chosachilikizidwa ndi Mawu a Mulungu, Baibulo.”

Anthu ambiri ayamikira kusanthula kwaukatswiri, kolembedwa bwino kumeneku kwa chiphunzitso chachikulu cha matchalitchi ambiri a Chikristu Chadziko. Ngati mungakonde kulandira kope la broshuwa imeneyi, chonde dzazani ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.

Ndingakonde kulandira broshuwa yamasamba 32 ya Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu? (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower yakwanuko kaamba ka chidziŵitso. Onani tsamba 2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena