Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w88 9/1 tsamba 32
  • Palibe Zondandaula Zowonjezereka Ponena za Nyimbozo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Palibe Zondandaula Zowonjezereka Ponena za Nyimbozo
  • Nsanja ya Olonda—1988
Nsanja ya Olonda—1988
w88 9/1 tsamba 32

Palibe Zondandaula Zowonjezereka Ponena za Nyimbozo

Anansi anali kudandaula ponena za nyimbo zoimbidwa kupyolera pa dongosolo lokuzira mawu pa sukulu ya makalasi a pansi mu Fukuoka Prefecture, Japan. Kenaka wachichepere anatenga makaseti a Kindom Melodies ku sukulu. Pambuyo pa kumvetsera ku iwo, mphunzitsiyo ananena kuti: “Izi ziri nyimbo zabwino. Mungaseŵere matepi amenewo pa dongosolo lokuzira mawu la sukulu.” Kuyambira pamenepo ophunzirawo, aphunzitsi, ndipo ngakhale anansiwo akhala akumvetsera ku Kingdom Melodies kwa mphindi 10 m’mawa mulimonse ndi mphindi 25 mkati mwa kupuma kwa pa chakudya cha masana. Ndipo sipanakhalenso zodandaula zowonjezereka ponena za nyimbozo!

Inu nanunso mungapindule kuchokera ku makonzedwe oimba odzetsa mpumulo amenewa. Iriyonse ya makasetiwo, Kingdom Melodies 1, 2, 3, 4, 5, 6, 7, ndi 8, iri kokha K16 ndipo ali ndi nthaŵi yoseŵera ya chifupifupi ora limodzi. Landirani makasetiwo amene andandalitsidwa pansipa mwa kudzaza ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, (ma)kaseti ochongedwa pansipa. Kaamba ka kaseti iriyonse yowodedwa, ndatsekeramo K16 (Zambia) kukwaniritsa pa zotaikazo.

□ Kingdom Melodies 1 □ Kingdom Melodies 2 □ Kingdom Melodies 3 □ Kingdom Melodies 4

□ Kingdom Melodies 5 □ Kingdom Melodies 6 □ Kingdom Melodies 7 □ Kingdom Melodies 8

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena