Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w88 5/1 tsamba 32
  • Anayamikiridwa ndi Dokotala wa Zamankhwala

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anayamikiridwa ndi Dokotala wa Zamankhwala
  • Nsanja ya Olonda—1988
Nsanja ya Olonda—1988
w88 5/1 tsamba 32

Anayamikiridwa ndi Dokotala wa Zamankhwala

Dokotala wa zamankhwala mu Frankfurt, West Germany, yemwe anaitanidwa kulembetsanso kulembetsa kwake kwa magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!, sanatumize kokha ndalama kaamba ka kulembetsansoko koma analongosola kuti:

“Ndimazizwitsidwa nthaŵi zonse kupeza kuperekedwa kokulira chotere kwa nkhani zabwino kwambiri ndi zokondweretsa​—zambiri za izo zomwe ziri zosakhoza ngakhale kulongosoledwa ndi chipembedzo​—pamtengo wotsika chotere. Ngakhale kuti ndiri ndi nthaŵi yochepera kaamba ka inemwini, madzulo anga onse ankatsirizidwa kaŵirikaŵiri wotsekeredwa m’chipinda changa ndikuŵerenga magazini anu nditayatsa nyali. Kachiŵirinso, ndikupereka kuyamikira kotentha kaamba ka kuyesayesa kwanu.

Bwanji osasangalala ndi kuŵerenga magazini yabwino kwambiri imeneyi inueni? Inu mungakhale ndi magazini odzetsa phindu aŵiriwa akuperekedwa kunyumba kwanu mwa kudzaza ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.

Chonde tumizani kulembetsa kwa chaka chimodzi kaamba ka Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! Ndatsekeramo K48.00 (Zambia). (Kunja kwa Zambia, lemberani ku nthambi ya Watch Tower ya kwanuko kaamba ka chidziŵitso.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena