Baibulo Losavuta Kuŵerenga mu Zilembo Zazikulu
Pamwambapa pali kutulutsidwanso mu mlingo wa mtundu weniweniwo, wa kusindikizidwa kwa chofalitsidwa cha zilembo zazikulu cha New World Translation of the Holy Scriptures. Baibulo lonselo liri mu mavolyumu anayi, iriyonse ikumakhala ndi masamba oposa 1,200. Volyumu iriyonse iri ndi zilozero zopindulitsa, ndipo Volyumu 4 iri ndi concordance ya masamba 77.
Volyumu 1 imakwaniritsa Genesis mpaka 2 Samueli; Volyumu 2, 1 Mafumu mpaka Nyimbo ya Solomo; Volyumu 3, Yesaya mpaka Malaki; ndipo Volyumu 4, Mateyu mpaka Chivumbulutso. Volyumu iriyonse ndi K100 Baibulo lonse la mavolyumu anayi lidzatumizidwa kwa inu, titalipiriratu positi, pa K400 yokha.
Chonde sonyezani mwa kuika chizindikiro pa mabokosi osiyanawo kuti ndi volyumu iti kapena mavolyumu a Baibulo amene mukufuna, ndipo tumizani unyinji wosonyezedwawo.
[ ] Ndatsekeramo K100 (Zambia) kaamba ka Volyumu 1.
[ ] Ndatsekeramo K100 (Zambia) kaamba ka Volyumu 2.
[ ] Ndatsekeramo K100 (Zambia) kaamba ka Volyumu 3.
[ ] Ndatsekeramo K100 (Zambia) kaamba ka Volyumu 4.