Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w88 1/1 tsamba 32
  • Kupirira Pansi pa Chitsenderezo cha Mphamvu Yoposa Munthu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kupirira Pansi pa Chitsenderezo cha Mphamvu Yoposa Munthu
  • Nsanja ya Olonda—1988
Nsanja ya Olonda—1988
w88 1/1 tsamba 32

Kupirira Pansi pa Chitsenderezo cha Mphamvu Yoposa Munthu

Kodi mumadzimva kuti ichi ndi chimene mukuchita?

Anthu ambiri amatero. Ndipo iwo athandizidwa m’kudziŵa mmene ena akuchitira. Kalata yochokera ku Greenville, Texas, yolemberedwa ku Watchtower Society, inalongosola kuti: “Mowonadi ndimayamikira nkhani zenizeni za moyo za Akristu omwe apirira kuvutika kwambiri ndi cholinga chofuna kukhala okhulupirika. Zambiri zinali zokumana nazo zimene ndinaŵerenga ndi misozi ikutsika m’maso mwanga, monga mmene ndinawonera kuti kokha Yehova Mulungu wowona anali wokhoza kuwapulumutsa iwo kuchokera ku matsoka oterowo amene iwo analimo. Chimandipangitsa ine kukhala Mkristu wodzichepetsa ndi woyamikira pamene ndiŵerenga zimene iwo anapyolamo, ndipo linandithandiza ine kusalingalira mokulira ponena za inemwini kapena kukhala wadyera.”

1988 Yearbook of Jehovah’s Witnesses yadzazidwa ndi zokumana nazo za kaimidwe kolimba ka Akristu kaamba ka chilungamo mkati mwa nkhondo mu Korea ndi mkati mwa zaka za uchigawenga mu Ireland. Yearbook yaperekanso nkhani ya mbiri yakale ya Mboni za Yehova mu Costa Rica, ndiponso ndi chithunzi chamakono cha ntchito yawo pa dziko lonse.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, 1988 Yearbook of Jehovah’s Witnesses. Ndatsekeramo K8.00.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena