Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w87 8/1 tsamba 32
  • ”Ntchito Yotopetsa Yatheratu!”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ”Ntchito Yotopetsa Yatheratu!”
  • Nsanja ya Olonda—1987
Nsanja ya Olonda—1987
w87 8/1 tsamba 32

”Ntchito Yotopetsa Yatheratu!”

Anachitira ndemanga motero m’modzi wogwiritsira ntchito Watch Tower Publications Index 1930-1985. Iye akuwonjezera: “Ndikusiyana kotani nanga mmene phunziro laumwini liriri. . . . Sindivutika kufunafuna unyinji womwe ndikufuna kuwona mu nthawi yochepa chabe.”

Bukhu latsopanoli laika zolozerako za chofalitsidwa chirichonse chofalitsidwa ndi Watch Tower Bible and Tract Society kuyambira 1930. Mwakuligwiritsira ntchito ilo limodzi ndi laibulale yanu ya zofalitsidwa za Watch Tower, mungafupikitse njira yopezera chidziwitso chachindunji pa zikwi za zinkhani zenizeni, monga ngati:

◻ chidzudzulo chofunika kutsatiridwa ndi chosafunikira kutsatiridwa m’kuphunzitsa mwana

◻ mmene mungakonzekerere kaamba ka kufunsidwa kwa ntchito

◻ ntchito ya DNA mu kuchulukitsa kwa maselo

◻ chimene pemphero siliyenera kuphatikizamo

◻ kawonedwe ka Chikristu pa kuletsa kubala

◻ zinsinsi za chovala chocheutsa

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, Watch Tower Publications Index 1930-1985. Ndatsckeramo K56. 00. Dzina

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena