Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w87 7/1 tsamba 32
  • “Makope Kaamba ka Mabwenzi Aumwini”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Makope Kaamba ka Mabwenzi Aumwini”
  • Nsanja ya Olonda—1987
Nsanja ya Olonda—1987
w87 7/1 tsamba 32

“Makope Kaamba ka Mabwenzi Aumwini”

Chifukwa chakuti anasangalala kotero ndi bukhu la Kupangitsa Moyo Wanu wa Banja Kukhala Wachimwcmwe, ambiri anagawana makopewo ndi ena. Mwachitsanzo, munthu wochokera ku Indiana, U. S. A. , akulemba:

“Ndingakonde kukuyamikirani pa bukhu loizwitsa kwambiri lomwendangowerenga kumene, Kupangitsa Moyo Wanu wa Banja Kukhala Wachimwcmwe. Ilo liri bukhu lolembedwa bwino ndi lokhweka kulimvetsetsa, ndipo anthu athu achichepere limodzinso ndi achikulire akapindula kuchokera ku kuwerenga ilo.

“Ndingakonde makope owonjezereka kaamba ka mabwenzi aumwini, ndipo ndingakondenso kugwiritsira ntchito bukhulo monga mphatso ya paukwati.

“Ndiri wa chikhulupiriro cha Chinazarene . . . ndipo sindingayamikire zinthu zakuthupi, kuposa bukhulo, kutumizidwa kwa ine . . . ngati chingakhale chotheka kwa ine kugula makope khumi a bukhulo pa mtengo wabwino, ndingayamikire kumva kuchokera kwa inu.”

Mwinamwake mumamva ponena za bukhu la Banja m’njira yofanana ndi mmene munthuyu achitira. Kodi mumadziwa wina wake amene mungagawanc naye ilo? Bwanji osamutumizira munthuyo kope la mphatso? Mungachite tero mwa kungodzaza ndi kutumiza kapepala kotsatiraka, ndi kungotsekeramo K8. 00 yokha limodzi ndi kapepalaka.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, bukhu la chikuto cholimba, la masamba 192 Kupangitsa Moyo Wanu wa Banja Kukhala Wachimwemwe limodzi ndi kalata yolongosola kuti iri mphatso yochokera kwa ‐‐‐‐‐‐‐‐‐‐‐‐‐

Ndatsekeramo K8. 00.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena