Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Mayankho a Mafunso 10 Omwe Achinyamata Amadzifunsa
Mayina a achinyamata ena amene mawu awo ali m’kabukuka tawasintha.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
March 2016 Printing
Chichewa (ypq-CN)
© 2016
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania