Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Gulu Lochita Chifuniro cha Yehova
“Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga.”—Sal. 40: 8.
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’bukuli akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu November 2019
Chichewa (od-CN)
© 2005, 2015, 2019
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA