Za M’katimu
TSAMBA MUTU
5 1 Madalitso Akuru Ali Pafupi Kwenikweni!
11 2 Cifukwa Cace Muyenera Kuciyesa Cipembedzo Canu
27 4 Cifukwa Cace Timakalamba ndi Kufa
46 6 Yesu Kristu, kupyolera mwa Amene Mulungu Adzawadalitsa Anthu
65 8 Ncifukwa Ninji Mulungu Wakulola Kuipa Kupitirizabe Mpaka Lero?
75 9 Cifukwa Cace Cimene “Kagulu Kankhosa” Kamapita Kumwamba
82 10 Ufumu wa Mulungu Uyamba Kulamulira Pakati pa Adani Ace
94 11 Masiku Otsiriza a Dongosolo Ili la Zinthu
102 12 Ulamuliro Wolungama Udzampangitsa Paradaiso
114 13 Carici Coona ndi Maziko Ace
122 14 Mmene Mungacidziwire Cipembedzo Coona
140 16 Miyambo Yofala Yosamkondweretsa Mulungu
151 17 Mmene Mungapemphelere ndi Kumvedwa
157 18 Kumvera Lamulo Kwacikristu
163 19 Kulemekeza Moyo ndi Mwazi Mwaumulungu
170 20 Kumaumanga Moyo Wabanja Wacimwemwe
181 21 Cosankha Canu ca Kumtumikira Mulungu
187 22 Kulambira Koona—Njira ya Moyo
Kusiyapo kokha ngati kwasonyezedwa, Malemba amene achulidwa m’bukhu ili ali ocokera mu Baibulo la Revised Union Nyanja Version.
Zidule za maina a Mabaibulo ena Acingelezi amene agwidwa mau:
AT — The Bible: An American lotembenuzidwa ndi J. Smith ndi E. Goodspeed, la 1935.
AV — Authorized or King James Version Bible, la 1611.
Dy — Roman Catholic Douay Version, la 1610.
NW — New World Translation of the Holy Scriptures, kusindikiza kobwerezedwanso kwa mu 1961.