Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g18 No. 2 tsamba 16
  • Mfundo Zina Zothandiza Mabanja

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfundo Zina Zothandiza Mabanja
  • Galamukani!!—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Mfundo Zina Zothandiza Makolo
    Galamukani!—2019
  • Mungapeze Thandizo
    Galamukani!—2020
  • Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?
    Kodi Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo Tingawapeze Kuti?
  • Kulemekezana M’banja
    Galamukani!—2024
Onani Zambiri
Galamukani!!—2018
g18 No. 2 tsamba 16
Akuona pa jw.org pogwiritsa ntchito tabuleti

Mfundo Zina Zothandiza Mabanja

BAIBULO LIMAPEREKA MALANGIZO OTHANDIZA KWAMBIRI kwa anthu okwatirana, makolo komanso kwa achinyamata. Malangizo ake angakuthandizeni kukhala oganiza bwino komanso kusankha bwino zochita.​—Miyambo 1:1-4.

BAIBULO LIMAYANKHANSO MAFUNSO OFUNIKA KWAMBIRI MONGA:

  • Kodi cholinga cha moyo n’chiyani?

  • Kodi Mulungu ndi amene amachititsa kuti tizivutika?

  • Kodi chimachitika n’chiyani tikamwalira?

Tikukulimbikitsani kuti mufufuze m’Baibulo mayankho a mafunso amenewa komanso ena. Onerani kavidiyo kakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? popanga sikani kachidindo aka kapena pitani pa www.jw.org.

Kuti mupeze nkhani zina zokhudza mabanja, werengani nkhani za mutu wakuti “Mfundo Zothandiza Mabanja” pa jw.org kapena pangani sikani kachidindo aka

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena