Zamkatimu
July 8, 2005
Mmene Mungapezere Ntchito ndi Kukhalitsa Pantchitopo
Masiku ano vuto la ulova lakula kwambiri chifukwa ntchito zikusowa zedi. Kodi mungatani kuti mupeze ntchito ndi kukhalitsa pantchitopo?
4 Mfundo Zisanu Zomwe Zingakuthandizeni Kupeza Ntchito
10 Zimene Mungachite Kuti Mukhalitse Pantchito
14 Ndinafunitsitsa Kukwanitsa Cholinga Changa
16 Mbiri ya Mawotchi a Pamkono
19 Kodi Kuba M’masitolo Ndi Nkhani Yaikulu Bwanji?
20 N’chifukwa Chiyani Anthu Amaba M’masitolo?
22 Kodi Ndani Amavutika Chifukwa cha Kuba M’masitolo?
25 Mmene Munthu Angasiyire Kuba M’masitolo
27 ‘Ndinkafuna Kuchidziwa Bwino Chipembedzo Changa’
31 “Pa Chilankhulo Chathu Palibe Mawu Otukwana”
32 Dziwani Zimene Baibulo Limaphunzitsa
Kodi Muyenera Kuopa Armagedo? 12
Pali zinthu zambiri zomwe anthu amakhulupirira zokhudza Armagedo zomwe si zoona. Kodi Armagedo yotchulidwa m’Baibulo muyenera kuiona bwanji?