Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g90 11/8 tsamba 2
  • Tsamba 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tsamba 2
  • Galamukani!—1990
Galamukani!—1990
g90 11/8 tsamba 2

Tsamba 2

PAKALI PANO, tonsefe ndife otanganitsidwa kupanga magwero amene amayendetsa indasitale yawo. Inuyo mukupanga chinachake chimene iwo akuchifuna. Kodi “iwo” amenewo ndani? Nkhokwe zosungirako mwazi ndi malo apakati osonkhanitsa plasma.

Anthu ambiri amakhulupirira kuti indasitale yamwazi imangofuna kupulumutsa miyoyo. Koma zonena zomachulukachuluka za osuliza zikupereka mlandu wakuti kusunga mwazi kwangokhala kokha bizinesi ina yaikulu. Chotero, kwenikweni, maselo a mwazi amakhala ndalama.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena