Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g87 10/8 tsamba 13
  • Kusakaza Kokulira kwa Fodya mu Greece

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kusakaza Kokulira kwa Fodya mu Greece
  • Galamukani!—1987
  • Nkhani Yofanana
  • Mliri wa Padziko Lonse
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Kodi Mawu a Mulungu Amati Chiyani pa Nkhani ya Kusuta Fodya?
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Ndudu za Fodya Kodi Mumazikana?
    Galamukani!—1996
  • Fodya ndi Kusanthula
    Galamukani!—1989
Onani Zambiri
Galamukani!—1987
g87 10/8 tsamba 13

Kusakaza Kokulira kwa Fodya mu Greece

AKUMAKULITSA pa mutu womveka wa nyimbo ya Chigriki, wochitira ripoti analemba ndi mawu ogwira mtima kuti: “Inde, ‘Grisi Sakufa,’ koma Agriki amafa.”

“Anthu zikwi khumi amafa chaka chirichonse chifukwa cha kusuta, m’dziko lathu lokha,” inachitira ripoti tero nkhani mu nyuzipepala ya Chiathenian Eleftheros Typos. Ena amakhulupirira kuti kusakaza kowona kokulira kwa fodya kungakhale kokulira kuwirikiza kaŵiri. Greece liri dziko lolima fodya, ndipo kusuta kuli chizoloŵezi chomakulakulabe pakati pa Agriki mosasamala kanthu za maripoti ambiri omwe alembedwa posachedwapa onena za ngozi yochititsidwa ndi kusuta.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena